Isaiah 8
14 "Iye adzakhala malo otetezeka! Koma kumbali zonse ziwiri za Isiraeli, adzakhala mwala woti anthu adzaphunthwapo! Mwala womwe udzawagwetse! Kwa anthu a mu Yerusalemu, adzakhala ngati msampha wokonzeka kuwakola!"
16 Mangani uthengawu! Mumatse chiphunzitsochi pakati pa omvera anga!