Isaiah 1
10 Imvani zomwe Yawe akunena, inu atsogoleri a Sodomu! Mverani zomwe Mulungu wathu akuphunzitsa, inu anthu a ku Gomora!
21 Mzinda womwe unali wokhulupirika wasanduka mkazi amene amagona ndi aliyense! Unali wodzaza ndi anthu amene ankachita zoyenera! Chilungamo chimakhala m'kati mwa makoma ake! Koma tsopano opha anthu amakhala kumeneko!