Isaiah 5

1 Ndikufuna kuyimbira nyimbo wokondedwa wanga! Nyimbo ya wokondedwa wanga ndi munda wake wa mphesa! Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mphesa! Unali paphiri la dothi lachonde!