Deuteronomy 31
7 Mose anaitana Yoswa kuti aimirire pamaso pa Isiraeli yense. Anamuuza kuti, "Khala wamphamvu! Limba mtima! Udzatsogolera anthu awa kulowa m'dziko limene Yahweh analonjeza kupatsa atate awo. Udzawathandiza kulitenga kuti likhale lawo."
9 Mose analemba lamulo ili. Analipereka kwa ansembe a fuko la Levi, amene amanyamula bokosi la chipangano cha Yahweh. Analiperekanso kwa atsogoleri onse achikulire a Isiraeli.
30 Mose anayankhula mawu onse a nyimbo iyi kwa Isiraeli yense. Kuyambira mawu oyamba mpaka otsiriza.