Isaiah 63
7 Ndidzanena za chikondi chokhulupirika chimene Yahweh wasonyeza. Ndidzatamanda Yahweh pa chilichonse chimene wachita. Ndidzalankhula za ubwino waukulu umene anapereka kwa Isiraeli. Anawaonetsa chifundo chochuluka kwambiri. Anakhuthula chikondi chochuluka.