Isaiah 50
4 Ambuye Yahweh anandipatsa mawu a munthu wophunzitsidwa bwino. Tsopano ndikhoza kulankhula ndi kulimbikitsa anthu omwe atopa. M'mawa uliwonse amandidzutsa. Amatsegula makutu anga kuti ndimvere ngati wophunzira wabwino.