Isaiah 41

8 Yahweh akuti, "Koma iwe, Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga! Yakobo, ndinakusankha! Ndinu ana a Abulahamu, amene ndinamutcha mzanga!"