Isaiah 38

1 Pa nthawi yomweyi, Hezekiya anadwala kwambiri. Anatsala pang'ono kufa. Mneneri Yesaya, mwana wa Amozi, analowa kuti amuwone. Yesaya anati, "Yehova akuti, 'Konza zinthu za m'nyumba mwako. Ufa. Suchira.'"

4 Kenako Yehova analankhula mawu ake kwa Yesaya.

7 "'Chizindikiro chako chochokera kwa Yehova ndi ichi. Chizindikiro ichi chidzatsimikizira kuti Yehova adzachita zomwe walonjeza.'"