Isaiah 36

1 Chaka chakhumi ndi chinayi cha ulamuliro wa Mfumu Hezekiya. Senakeribu, mfumu ya Asiriya, anabwera ndikumenya mzinda uliwonse wokhala ndi mpanda mu Yuda. Ndipo anawagonjetsa onse.