Isaiah 30
1 Yahweh akuti, "Ululu ukubwera kwa ana anga a mitu yowuma! Amapanga mapulani koma sandifunsa! Amapanga mapangano popanda Mzimu wanga! Amunjika tchimo pamwamba pa tchimo!"