Isaiah 28
16 Moti Ambuye Yahweh akuti: "Ndikuika mwala mu Ziyoni! Mwala wapanthiti womwe wayesedwa! Mwala wapangodya, wolimba komanso wokhulupirika! Yense wokhulupirira sadzathawa mwamantha!"