Deuteronomy 29

1 Ili ndi pangano. Awa ndi mawu amene Yahweh anauza Mose kuti ayankhule kwa Isiraeli m'dziko la Mowabu. Izi zinabwera pamwamba pa lonjezo lomwe anapanga pa Phiri la Horebu.