Genesis 8
1 Koma Mulungu anakumbukira Nowa. Anakumbukira nyama zomwe zinali m'chombo. Mulungu anatumiza mphepo yamphamvu pa dziko lapansi. Pang'onopang'ono, madzi anayamba kuchepa.
8 Kenako Nowa anatumiza nkhunda. Ankafuna kuona ngati madzi achepa.
10 Anadikira masiku ena asanu ndi awiri. Kenako anatumizanso nkhundayo.
18 Nowa anatuluka panja pa dzuwa. Ana ake anamutsatira. Mkazi wake anatuluka. Akazi a ana ake anatuluka.