Genesis 50

4 Kulira kutatha, Yosefe anapita kwa anthu omwe ankatumikira Farao. "Ngati ndili wofunika kwa inu, mukandiperekere uthenga uyu kwa Farao."

10 Anafika pamalo otchedwa Atadi. Patawoloka Mtsinje wa Yorodani. Kumeneko analira kwambiri mofuula ndi chisoni chachikulu. Yosefe analirira bambo wake masiku asanu ndi awiri mosalekeza.

12 Ana a Yakobo anachita zonse zimene anawauza.

15 Bambo wawo anamwalira. Abale a Yosefe anachita mantha ngati mthunzi uli pa iwo. "Bwanji ngati Yosefe wakhala akudikirira? Bwanji ngati abwezera zonse zimene tinamuchitira?"

24 Yosefe anaitana abale ake. "Nthawi yanga ikuthera. Koma Mulungu akukukumbukirani! Adzabwera! Adzakutsogolerani potuluka m'dziko lino ndikukuperekezani ku dziko lomwe analonjeza kwa Abulahamu, Isake ndi Yakobo!"