Genesis 5
1 Uwu ndi mndandanda wa banja la Adamu. Pamene Mulungu anapanga anthu oyamba, anawapanga kuti azifanana ndi Iye.
21 Inoki anakhala pa dziko lapansi zaka 65. Kenako mwana wamwamuna anabwera. Anamutcha Metusela.
28 Lameki anakhala pa dziko lapansi zaka 182. Kenako mwana wamwamuna anabwera.