Genesis 47
1 Yosefe anapita kwa Farao. Anati, "Abambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani! Abweretsa nkhosa zawo, ng'ombe zawo, ndi chilichonse chomwe ali nacho. Pakali pano ali ku Goseni."
11 Yosefe anapatsa abambo ake ndi abale ake malo ku Iguputo. Anawaika pamalo abwino kwambiri. Linali dziko la Ramese. Farao ananena kuti atha kutenga malowo.