Genesis 38
1 Nthawi imeneyo, Yuda anasiya abale ake. Anapita kukakhala ndi mzake dzina lake Hira waku Adulamu.
6 Yuda anamufunira mkazi mwana wake woyamba Eri. Dzina lake anali Tamara.
12 Zaka zinapita. Mkazi wa Yuda anamwalira. Yuda ataleka kulira, anapita ku Timina kukameta ubweya wa nkhosa zake. Mzake Hira anapita naye.
20 Yuda anatumiza mbuziyo m'manja mwa mzake Hira. Hira anapita kukatenga zinthu zija kwa mkaziyo. Koma sanamupeze.