Genesis 23

1 Sara anakhala ndi moyo zaka zana limodzi mphambu makumi awiri ndi zisanu ndi ziwiri. Kenako nthawi yake inatha.

3 Misozi yake itatha, Abrahamu ananyamuka kuchoka pamtembo wa mkazi wake. Analankhula kwa Ahiti amene ankakhala kumeneko.