Genesis 18
1 Yahweh anaonekera pa mitengo ikuluikulu pafupi ndi Mamre. Abrahamu anakhala pakhomo la hema wake. Dzuwa linkatentha kwambiri kuchokera mmwamba.
16 Amunawa anaimirira. Anayang'ana kumbali ya Sodomu. Abrahamu anayenda nawo pofuna kuwaperekeza.
22 Amunawa anatembenuka ndikuyamba ulendo wopita ku Sodomu. Koma Abrahamu anatsala, ataimirira pamaso pa Yahweh.
26 Yahweh anati, "Ngati ndipeza anthu abwino makumi asanu mu Sodomu, ndidzapulumutsa mzinda wonse chifukwa cha iwo."