Genesis 10
1 Awa ndi ana omwe Nowa anali nawo: Semu, Hamu, ndi Yafeti. Pambuyo pa chigumula, onsewo anabereka ana amuna.
8 Kusi anali ndi mwana wamwamuna wina. Nimurodi. Mnyamatayu anakula n'kukhala wankhondo. Wankhondo woyamba wamkulu kwambiri yemwe dziko linamuona.